M D F AIR

M D F AIR Malawi army defence forces

24/11/2022

Lelo tikambepo zomwe naziwona my first mission mdziko la democratc of congo..tsiku lama bullets .fire to fire . no mercy times^ pepani ndingonena modula dula due to M .D. F. PORICY... Tinapita gulu la ma soldiers i mean ochokera ma base osiana dziko muno ,sitinganene figure ya anthu kma ineo nditamalize bwn bwn as a sniper ..ndinauzidwa bwn bwn za mphepo ,distance .cumpus kmanso kuyang'anitsitsa mosaona nyengo ... gulu lotchedwa M 23 LABELS la dziko la DRC linali GULU loopsya ngakhale zida zomwe amagwilitsa ntcito kmanso muzonse as u knw ma afrcans .Sometimes u may a shoot a
person bt not dead... Are u followng .. Tipitilze

07/11/2022

Thanks kwa anthu omwe ma panga follow up this group. Dziwani kt musamadikile nthawi yomwe izatuluke vaccancy then inuo mkulembela ayii makalata antchito ku MALAWI DFNC FC amabwela nthawi ilionse ena mwai wao umagwela munthaw yomwe samaembekezela kt akhoza kutengdwa kudzayamba nawo ma training...Kma dziwa osapeleka ndalama kwa munthu emwe angakunamizeni kt akulembetsani ntchito dziwani ndi bodza .Chonde pewani izi.

10/10/2022

Soon we're going to s
Post a WhatsApp link
But be careful

Address

Lilongwe

Telephone

+265888308000

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when M D F AIR posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to M D F AIR:

Share