16/05/2024
Follow and subscribe on this YouTube channel https://www.youtube.com/
Pomwe muziphuzirako ti ntchito Tina tosafuna mechanic kuti mpaka akupezeni pakhomo
Ngati kudziwa ngati alternator yanu ikuchager
Kusotha nyali
Kupanga ka A service
Ndi kuphuziraso mmene mungazitetezere safety pamene mukupanga zithu zomwe mutaphuzire ma videos aziponyedwe ku channel imeneyi
Chachikulu pangani open and subscribe
https://www.youtube.com/
The mechanic from the lake malawi . Remember to subscribe