Afri Tech Motors

Afri Tech Motors We repair AUTOMATIC GEARBOX , engine rebuild, Diagnosis, suspension, auto electrical,welding and pan

18/07/2026
10/04/2026
Many people started hating this beautiful product on motor industry, This is Mazda CX5, with 2.2 SH Diesel engine, today...
11/02/2026

Many people started hating this beautiful product on motor industry, This is Mazda CX5, with 2.2 SH Diesel engine, today I want to convince those who bought this machine and the ones who dreams to buy.
Mazda CX5 SH,SUV diesel, very luxury and comfortably plus stability,
Galimoto siimatha ayi koma zimatha ndi ndalama, ndipo Masiku ano palibe galimoto yobvuta ayi koma zimabvuta ndi mechanical.
Anthu ambiri akudandaula akuti galimoto yobvuta , koma ili ndi bonza, bvuto kukumana ndi munthu oti galimoto yi amaifuna koma akulephera kugula,ndie amakhala ndi ka mtima ka nsanje,

Ndipo anthu ambiri akupanga blame engine overheating ndi twin turbo problem, izo ndi zoona koma is not permanent problem ayi, ndi zinthu zoti ukakhala ndi ndalama ndi zokhonzedwa ndithu, and mabvuto a wawa amapezeka ma galimoto onse,,

Ndipo anthu ambiri akumanena kuti ndi galimoto yobvuta kukhonza pakakhala mabvuto a engine ndi twin turbo, izo ndi zoona koma zimatengera ndi technician yemwe akukhonza, I always advice all members ya KYC kuti chonde pititsani galimoto yanu kwa mechanic oyenera osati mutsatile chifukwa cha cheaper ayi, galimoto ya 40 million mwagula nokha ma spare parts a 1 million koma mukufuna mechanical kufuna kumpatsa 30pin, Tiyeni tiwakonde a mechanic anthu nawo ndi anthu ngati ife,,,
Ngati muli ndi mabvuto a engine overheating Kapena twin turbo, bwerani tikukhonzereni , brand new twin turbo available,visit our workshop Manja next st Columba church. Afri Tech motors ,page Or
[email protected]

Address

Blantyre

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Afri Tech Motors posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Afri Tech Motors:

Shortcuts

Share