Yota mechanic

Yota mechanic Motor vehicle mechanics

14/12/2025

Mazda. CX3 and CX5 mwayirandira bwanji

14/12/2025

MAZDA CX3 and CX5 eeeeeeeeeeee anapanga

14/12/2025

ZIFUKWA ZOMWE ZINGAPANGITSE KUTI GALIMOTO YANU IZIMWA MAFUTA KWAMBIRI
1.Ngati air cleaner ili yakuda
2.Ngati ma spark plug atha
3.Ngati mukuyendera matayala akuphwa
4.Ngati ma coil sakupereka Moto okwanira
6.Ngati mukuyendera ma gear ochepa
7.Ngati mwanyamula katundu odutsa msinkhu wake
8.Ngati ma sensor monga Air flow sensor, throttle position sensor, oxygen sensor , calm shaft sensor ndi crankshaft sensor salibwino
9.Ngat throttle body ndi yakuda
10.Ngati mukuyendera idling ili pamwamba
11.Ngati ma tyres Aku binder
12.Ngati ma injectors saku faya momwe ayenera kuchitira or akumadontha APA ndapanga based kwambiri ma galimoto a petrol

Andi zina zotero ngati mufuna kudziwa zambiri zokhuza galimoto follow my page

ZOMWE ZINGAPANGITSE KUTI GALIMOTO YANU ISALIRE 1.Ngati mafuta mu tank mulibe 2.Ngati pump yamafuta silibwino 3.Ngati fue...
13/12/2025

ZOMWE ZINGAPANGITSE KUTI GALIMOTO YANU ISALIRE
1.Ngati mafuta mu tank mulibe
2.Ngati pump yamafuta silibwino
3.Ngati fuel filter ndiyakuda
5.Gati battery sili bwino
6.Ngati starter motor silibwino
7.Ngat ma sensors ena salibwino monga ngati camshafts sensor ndi crankshaft sensor
8.Ngat computer box silibwino
9.Ngati ma ground wire or tinene k*ti ma earthing salibwino
10.Ngati yaphonya timing
11.Ngati ndi ya automatic munayizimitsira mu drive
12.Ngati mafuse ena aphya

Ndi zina zambiri, Follow our page k*ti mudziwe zambiri

11/12/2025

Tchotsani umbuli pa zokhuza galimoto by following this page

11/12/2025

Ma mechanic ngati mukufuna kudziwa zagalimoto follow this page ndipo Ku school zinthu sizikuvutani

11/12/2025

Follow this page for you to know more about car

09/12/2025

With Memo Makanika – I just made it onto their weekly engagement list by being one of their top engagers!

09/12/2025

LANGIZO LIMODZI KWA OMWE MULI NDI GALIMOTO ZA TURBOCHARGER;
Muzionetsetsa k*ti air cleaner isamakhare yakuda ngati m'mene amapangira zinazi ,chifukwa chimozi mwa zomwe zimaononga turbocharger ndi ma air cleaner akuda DZIWANI k*t turbocharger ndiyodula kuposa air cleaner

Sinthan oil k*ti galimoto yanu ikhare nthawi yayitali musanamasile engine
09/12/2025

Sinthan oil k*ti galimoto yanu ikhare nthawi yayitali musanamasile engine

Address

0885092673
Mzuzu

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Yota mechanic posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share