Nyasahotline265brings

Nyasahotline265brings NEVER DESIGN YOUR CHARACTER AS A GARDEN WHERE EVERYONE CAN WALK.

🚨😁 Eli Njuchi akuti dzulo usiku athu Ena achipongwe anapanga hack page  Yake Ndikuyamba kulemba zosakhara bwino...
05/06/2026

🚨😁 Eli Njuchi akuti dzulo usiku athu Ena achipongwe anapanga hack page Yake Ndikuyamba kulemba zosakhara bwino.... Komanso zonyoza Nyimbo yatsopano imene Namadingo watulutsa.

Ngakhale izi zili chomwechi athu ena amene amatsata Makina a computer akuti kumakhala kovuta kuti page imene ili Verified Kuti ipangidwe Hack..

zimene zikupeleka Chikayikiro kuti Mwina Nkutheka zithu zonyoza zimenezi zinalembedwadi Ndi Mwiniwakeyo😅

🚨😁 Phyzix akuti zomamutchura kuti“PhunguManyizo”zitheretu Ndipo sizikumusangalatsa....otherwise Dzina limeneli wina alan...
30/05/2026

🚨😁 Phyzix akuti zomamutchura kuti
“PhunguManyizo”zitheretu Ndipo sizikumusangalatsa....otherwise Dzina limeneli wina alandirana Nazo Makofi 😅🤝🏾!!

🚨🔥 “ALENDO AKACHOKA, NTCHITO ZIPEZEKA?” — MALema AFUNSA FUNSO LOMWE LAGWEDERA SOUTH AFRICA 🇿🇦🇬🇭😳Anthu 300 a ku Ghana ath...
30/05/2026

🚨🔥 “ALENDO AKACHOKA, NTCHITO ZIPEZEKA?” — MALema AFUNSA FUNSO LOMWE LAGWEDERA SOUTH AFRICA 🇿🇦🇬🇭😳

Anthu 300 a ku Ghana athawa ku South Africa pa ndege yapadera kuchokera ku Johannesburg kupita ku Accra chifukwa cha mantha ndi kuzunzidwa. ✈️💔

Kwa milungu ingapo, ma protest odana ndi alendo akhala akuchitika, pomwe ena akuwadzudzula kuti ndi amene akubweretsa ulova ndi mavuto azachuma. ⚠️📉

Koma mtsogoleri wa Julius Malema wapereka mawu omwe akufalikira kwambiri pa social media:

🗣️ “Anthu 300 a ku Ghana achoka… ndiye ntchito 300 zapangidwa?” 😳🔥

Funso limeneli lakhudza anthu ambiri chifukwa likuwonetsa kuti mwina alendo akungopangidwa scapegoat pa mavuto akulu a chuma. 🌍💔

🇬🇭 Anthu omwe abwerera ku Ghana akuti sanalinso otetezeka m'mabizinesi awo ndi m’nyumba zawo.

🇬🇭 Minister wa Foreign Affairs wa Ghana Samuel Okudzeto Ablakwa wati zimene zikuchitikazi ndi “zodetsa nkhawa kwambiri.”

⚠️ Malema anachenjeza kuti: "Obwela onse akachoka ndipo ntchito zikamasowabe… kodi anthu adzayamba kudzudzula ndani?” 😔🔥

Kuti Zisamakuophonyeni follow Ving Blessing Bananna

Lord, if I’m chasing the wrong things, redirect me.
30/05/2026

Lord, if I’m chasing the wrong things, redirect me.

😭😭💔💔Lero kulira mawa kulira tili munyengo zosiliza abale  azimayi kuyipa mtima kwabwanji uku?😭😭😭😭😭😭💔💔💔Zachitika dzulo ma...
26/05/2026

😭😭💔💔Lero kulira mawa kulira tili munyengo zosiliza abale azimayi kuyipa mtima kwabwanji uku?😭😭😭😭😭😭💔💔💔
Zachitika dzulo madzulo
Nkhaniyi ikuti bambo wina anatsanzika nkazi wake m'mawa kuti akupita kuchito nde kufika chamma 4:00pm pamene mkazi amaimba foni akuti imakana then mzimayiyu ananyanyala nde kufika chamma 5pm ndipamene bamboyi amatulukila kufika pa deni bottle la mowa lili mmanja anampeza nkazi wakeyu akudula anyezi kma zachisoni nkaziyi atangomuona mamunayu akuti anamudumphila uku mpeni wake uli m'manja nkuzamuhaga then kuvunga chi kiss bambo atakomedwa ndi hag anagwetsa bottle la wine 🍷🍷onse nkutaika pansi abale ndim'mene wadulira mowamu nde onse ungotayika ndipo bamboyi wadandaula kwambiri🙄😁😁😁😎

26/05/2026

andibwereke

26/05/2026

king of dancall

26/05/2026

sinzanyengaso

26/05/2026

🚨❤️ 1 V 1 Question Segment with Zeze 🤝🏾!!

Q1. If your Music Career didn’t work out...what would you be..?

✅ Zeze’s Response: A Soccer Player or Probably a Manager in a book store...coz I was selling books before.

Q2. Which Artist in Malawi would you love to collaborate with this year..!?

✅ Zeze’s Response: l’m cool with everybody...& I would really want to have a song with everybody...if that would make History.

Q3. What keeps you motivated when things are tough..!?

✅ Zeze’s Response: My wife & My Family

Q4. What’s one challenge... People don’t see behind the Music Industry.

✅ Zeze’s Response: one thing that people don’t see behind the music industry....is the ability of being able to switch up...uuh u know?....to adapt, to change, also to always be relevant ...yah that’s the thing that many people know behind this sh**t.

Q5. What’s one song do you want people to sing tonight..?

✅ Zeze’s Response: Eyo lero Ndilira Munvura zifukwa Ndizambiri sinditha kutchura😅

Credit: Sunlens Photography (MZUZU)

Nkhani ya mtsikana yu ku salima.Iyeyu ayika lero maliro ake, akuti mtsikanayu anali ndi mimba nde anamuuza kwao achotse ...
25/05/2026

Nkhani ya mtsikana yu ku salima.

Iyeyu ayika lero maliro ake, akuti mtsikanayu anali ndi mimba nde anamuuza kwao achotse yoyamba anachotsa...

Khalekhaleni nkukhalanso ndi ina yachiwiri kuchoka kwa chibwenzi chake chomwechonso, ndipo atamuuza bwenzi lake anamuuza kuti asunge adzalera onse mwana koma makolo ake atanva anamuuza achotsenso chifukwa cha school kuti apitilize, ndipo anamupatsa mankhwala okuti amwe ichoke.

Mimba ija itachoka anali ku chipatala chifukwa chonva ululu wazina zomwe zinatsalira mkati mwake. Atakhala kuchipatala kwa masiku ndithu anatuluka koma anamuuza kuti azikadya za soft kaye chifukwa anali fragile mkati mwake.

Atapita kunyumba chibwenzi chake chija chinamva kuti mimba ija wachotsa ndipo iye sizinamusangalatse nkumuuza kuti chibwenzi chatha.

Iyeyu atanva izi sizinamusangalatse ndipo anamwa paracetamol (Panadol wambiri oposa 20 panthawi imodzi) nkukakhala kutchire yekhayekha, anthu ena mkumuona nkumutengela kuchipatala komwe anakamwalira.

Sad

Kodi olakwa ndindani pankhaniyi?
Makolo?
Chibwenzi?
Or
Iyeyo?

Address

Blantyre

Opening Hours

Monday 09:00 - 17:00
Tuesday 09:00 - 17:00
Wednesday 09:00 - 17:00
Thursday 09:00 - 17:00
Friday 09:00 - 17:00
Saturday 09:00 - 17:00

Telephone

+27618704029

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Nyasahotline265brings posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Nyasahotline265brings:

Share